Yobu 15:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iye amalimbana ndi Mulungu mwamakani,Atatenga chishango chake cholimba komanso chochindikala.