-
Yobu 15:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Iye amakhala mʼmizinda imene idzawonongedwe,
Mʼnyumba zimene simudzakhala aliyense,
Zimene zidzakhale milu ya miyala.
-