Yobu 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndasoka ziguduli kuti ndibise khungu langa,+Ndipo ndakwirira ulemu wanga* mufumbi.+