Yobu 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chonde, landilani chikole changa ndipo muchisunge. Kodi pali winanso amene angagwirane nane chanza nʼkulonjeza kuti andithandiza?+
3 Chonde, landilani chikole changa ndipo muchisunge. Kodi pali winanso amene angagwirane nane chanza nʼkulonjeza kuti andithandiza?+