Yobu 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa cha kuzunzika, maso anga ayamba kuchita mdima.+Manja ndi miyendo yanga zakhala ngati mthunzi.
7 Chifukwa cha kuzunzika, maso anga ayamba kuchita mdima.+Manja ndi miyendo yanga zakhala ngati mthunzi.