-
Yobu 18:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ngakhale utadzikhadzulakhadzula chifukwa choti wakwiya,
Kodi dziko lapansi lingasiyidwe chifukwa cha iwe?
Kapena kodi thanthwe lingasunthe pamalo ake?
-