Yobu 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zoopsa zimamuchititsa mantha paliponse,+Ndipo zimamuthamangitsa zili naye pafupi kwambiri.