Yobu 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndilezereni mtima pamene ndikulankhula.Ndikamaliza kulankhula, mukhoza kuyamba kundinyoza.+