Yobu 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi madandaulo anga akupita kwa munthu? Zikanakhala choncho, kodi ndikanakhalabe woleza mtima?*