Yobu 21:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Dothi lamʼchigwa* limene adzamukwirire nalo lidzakhala lotsekemera kwa iye,+Ndipo anthu onse adzamutsatira*+Mofanana ndi anthu osawerengeka amene anapita iye asanapite.
33 Dothi lamʼchigwa* limene adzamukwirire nalo lidzakhala lotsekemera kwa iye,+Ndipo anthu onse adzamutsatira*+Mofanana ndi anthu osawerengeka amene anapita iye asanapite.