Yobu 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi zoti ndiwe wolungama, Wamphamvuyonse ali nazo ntchito?*Kapena kodi amapindula chilichonse chifukwa choti umachita zinthu mokhulupirika?+ Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:3 Nsanja ya Olonda,9/15/2005, tsa. 262/15/1995, ptsa. 27-28
3 Kodi zoti ndiwe wolungama, Wamphamvuyonse ali nazo ntchito?*Kapena kodi amapindula chilichonse chifukwa choti umachita zinthu mokhulupirika?+