Yobu 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Paja umalanda abale ako chikole popanda chifukwa,Ndipo anthu umawavula zovala zawo nʼkuwasiya ali maliseche.*+
6 Paja umalanda abale ako chikole popanda chifukwa,Ndipo anthu umawavula zovala zawo nʼkuwasiya ali maliseche.*+