Yobu 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anthu amene imfa inawatenga nthawi yawo isanakwane,*Amene maziko awo anakokoloka ndi madzi osefukira?*+
16 Anthu amene imfa inawatenga nthawi yawo isanakwane,*Amene maziko awo anakokoloka ndi madzi osefukira?*+