Yobu 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Landira malangizo ochokera pakamwa pake,Ndipo usunge mawu ake mumtima mwako.+