Yobu 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndikanadziwa kumene ndingapeze Mulungu,+ Ndikanapita kumalo kumene iye amakhala.+