-
Yobu 23:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Kumeneko, mlandu wa munthu wowongoka mtima udzaweruzidwa pamaso pake,
Ndipo Woweruza wanga adzagamula kuti ndilibe mlandu mpaka kalekale.
-