-
Yobu 23:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Nʼchifukwa chake ndikuda nkhawa ndi zimene Mulungu angandichitire.
Ndikaganizira za iye, ndikumachita mantha kwambiri.
-