Yobu 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Nʼchifukwa chiyani Wamphamvuyonse sanakhazikitse nthawi yachiweruzo?+ Nʼchifukwa chiyani anthu amene amamudziwa sanaone tsiku lake lachiweruzo?
24 “Nʼchifukwa chiyani Wamphamvuyonse sanakhazikitse nthawi yachiweruzo?+ Nʼchifukwa chiyani anthu amene amamudziwa sanaone tsiku lake lachiweruzo?