Yobu 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Osaukawo amakhala usiku wonse ali maliseche,+Amakhala pamphepo opanda chofunda.