Yobu 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mumdima anthu oipawo amathyola nyumba za anthu,Masana amadzitsekera mʼnyumba. Iwo amadana ndi kuwala.+
16 Mumdima anthu oipawo amathyola nyumba za anthu,Masana amadzitsekera mʼnyumba. Iwo amadana ndi kuwala.+