Yobu 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma iwo amatengedwa mwamsanga ndi madzi. Malo awo adzakhala otembereredwa.+ Sadzabwerera kuminda yawo ya mpesa.
18 Koma iwo amatengedwa mwamsanga ndi madzi. Malo awo adzakhala otembereredwa.+ Sadzabwerera kuminda yawo ya mpesa.