-
Yobu 24:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Mulungu adzagwiritsa ntchito mphamvu zake powononga anthu amphamvu.
Ngakhale atakhala ndi mphamvu, iwo sadziwa ngati angakhalebe ndi moyo kapena ayi.
-