Yobu 24:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mulungu amawalola kuti azidzidalira komanso kuti akhale otetezeka.+Koma maso ake amaona chilichonse chimene akuchita.*+
23 Mulungu amawalola kuti azidzidalira komanso kuti akhale otetezeka.+Koma maso ake amaona chilichonse chimene akuchita.*+