Yobu 27:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nyumba imene wamanga ndi yosalimba ngati ya kadziwotche,Ndiponso ngati chisakasa+ chimene mlonda wamanga.
18 Nyumba imene wamanga ndi yosalimba ngati ya kadziwotche,Ndiponso ngati chisakasa+ chimene mlonda wamanga.