-
Yobu 27:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Iye adzapita kukagona ali wolemera, koma chuma chake sichidzakhalitsa.
Akadzatsegula maso ake, padzakhala palibe chilichonse.
-