Yobu 27:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mphepo yakumʼmawa idzamunyamula nʼkumusowetsa,Ndipo idzamuchotsa pamalo pake.+