Yobu 28:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mulungu yekha ndi amene amadziwa njira yozipezera,Iye yekha ndi amene amadziwa kumene zimakhala.+