Yobu 29:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anthu ankandimvera ndipo ankandidikirira,Ankakhala phee kuyembekezera kuti amve malangizo anga.+