Yobu 30:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa Mulungu wandilanda zida* nʼkundipangitsa kuti ndikhale wopanda mphamvu,Iwo amachita zinthu modzikuza pamaso panga.
11 Chifukwa Mulungu wandilanda zida* nʼkundipangitsa kuti ndikhale wopanda mphamvu,Iwo amachita zinthu modzikuza pamaso panga.