-
Yobu 30:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Iwo aimirira kudzanja langa lamanja ngati gulu la anthu achiwawa kuti andiukire.
Amandichititsa kuti ndithawe,
Koma amanditchingira njira kuti andiwononge.
-