Yobu 31:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kodi ndinayamba ndanenapo zabodza? Kodi ndinayamba ndachitirapo aliyense zachinyengo?+