-
Yobu 31:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Kodi ndinachitapo mantha ndi zimene gulu la anthu lingachite,
Kapena ndinayamba ndaopa mawu onyoza a mabanja ena,
Nʼkundichititsa kukhala chete komanso kuopa kutuluka panja?
-