Yobu 31:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Zikanakhala bwino wina akanandimvetsera.+ Ndikanasainira dzina langa pa zimene ndanena.* Wamphamvuyonse andiyankhe.+ Zikanakhala bwino munthu amene akundiimba mlandu akanalemba milandu yanga papepala. Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 31:35 Nsanja ya Olonda,11/15/2005, tsa. 11
35 Zikanakhala bwino wina akanandimvetsera.+ Ndikanasainira dzina langa pa zimene ndanena.* Wamphamvuyonse andiyankhe.+ Zikanakhala bwino munthu amene akundiimba mlandu akanalemba milandu yanga papepala.