Yobu 32:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma Elihu mwana wa Barakeli, mbadwa ya Buza+ wamʼbanja la Ramu anakwiya kwambiri. Iye anakwiyira kwambiri Yobu chifukwa ankadziikira kumbuyo kuti iye ndi wolungama, osati Mulungu.+ Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:2 Nsanja ya Olonda,3/15/2006, tsa. 1511/15/1994, tsa. 17
2 Koma Elihu mwana wa Barakeli, mbadwa ya Buza+ wamʼbanja la Ramu anakwiya kwambiri. Iye anakwiyira kwambiri Yobu chifukwa ankadziikira kumbuyo kuti iye ndi wolungama, osati Mulungu.+