Yobu 32:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndakhala ndikukumvetserani mwachidwi,Koma palibe aliyense wa inu amene wapereka umboni wosonyeza kuti Yobu ndi wolakwa*Kapena kuyankha zonena zake.
12 Ndakhala ndikukumvetserani mwachidwi,Koma palibe aliyense wa inu amene wapereka umboni wosonyeza kuti Yobu ndi wolakwa*Kapena kuyankha zonena zake.