Yobu 33:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mnofu wake umatha, osaonekanso,Ndipo mafupa ake amene samaoneka, amakhala pamtunda.*