Yobu 33:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Adzapemphera kwa Mulungu+ ndipo iye adzamukomera mtima,Adzaona nkhope yake akufuula mosangalala,Ndipo Mulungu adzayambanso kuona munthuyo kuti ndi wolungama.
26 Adzapemphera kwa Mulungu+ ndipo iye adzamukomera mtima,Adzaona nkhope yake akufuula mosangalala,Ndipo Mulungu adzayambanso kuona munthuyo kuti ndi wolungama.