Yobu 35:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiye kodi iye angamvetsere mukamadandaula kuti simukumuona?+ Iye ndi amene angaweruze mlandu wanu, choncho muzimuyembekezera.+
14 Ndiye kodi iye angamvetsere mukamadandaula kuti simukumuona?+ Iye ndi amene angaweruze mlandu wanu, choncho muzimuyembekezera.+