Yobu 36:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye sadzateteza moyo wa anthu oipa,+Koma amachitira chilungamo anthu amene ali pamavuto.+