Yobu 36:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye amakukokani mukatsala pangʼono kukumana ndi mavuto+Nʼkukupititsani pamalo otakasuka, opanda mavuto.+Patebulo panu pali chakudya chambiri chabwino chimene chimakusangalatsani.+
16 Iye amakukokani mukatsala pangʼono kukumana ndi mavuto+Nʼkukupititsani pamalo otakasuka, opanda mavuto.+Patebulo panu pali chakudya chambiri chabwino chimene chimakusangalatsani.+