Yobu 36:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndi ndani anauzapo Mulungu kuti chitani izi,+Kapena ndi ndani amene anamuuza kuti, ‘Zimene mwachitazi ndi zolakwikaʼ?+
23 Ndi ndani anauzapo Mulungu kuti chitani izi,+Kapena ndi ndani amene anamuuza kuti, ‘Zimene mwachitazi ndi zolakwikaʼ?+