Yobu 39:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nthiwatiwa imakupiza mapiko ake mosangalala,Koma kodi mapiko ndi nthenga zake nʼzofanana ndi za dokowe?+
13 Nthiwatiwa imakupiza mapiko ake mosangalala,Koma kodi mapiko ndi nthenga zake nʼzofanana ndi za dokowe?+