Yobu 39:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kodi ndi iwe amene umapereka mphamvu kwa hatchi?+ Kodi ndi iwe amene umaveka khosi lake manyenje awirawira?
19 Kodi ndi iwe amene umapereka mphamvu kwa hatchi?+ Kodi ndi iwe amene umaveka khosi lake manyenje awirawira?