Yobu 39:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Imanyoza mantha ndipo siopa chilichonse.+ Sibwerera mʼmbuyo chifukwa choopa lupanga. Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 39:22 Nsanja ya Olonda,1/15/2006, ptsa. 14-15