Yobu 39:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Lipenga likangolira imati, ‘Eyaa!’ Imanunkhiza nkhondo ili kutali,Ndipo imamva kufuula kwa atsogoleri a asilikali komanso phokoso la nkhondo.+ Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 39:25 Nsanja ya Olonda,1/15/2006, ptsa. 14-15
25 Lipenga likangolira imati, ‘Eyaa!’ Imanunkhiza nkhondo ili kutali,Ndipo imamva kufuula kwa atsogoleri a asilikali komanso phokoso la nkhondo.+