Yobu 40:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mafupa ake ali ngati mapaipi akopa,*Miyendo yake ili ngati ndodo zachitsulo.