Yobu 40:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mtsinje ukadzaza, iyo sichita mantha. Imalimba mtima ngakhale madzi a mu Yorodano+ atasefukira nʼkumaimenya kumaso. Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 40:23 Nsanja ya Olonda,11/15/1994, tsa. 19
23 Mtsinje ukadzaza, iyo sichita mantha. Imalimba mtima ngakhale madzi a mu Yorodano+ atasefukira nʼkumaimenya kumaso.