Yobu 41:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kodi ungabowole chikopa chake ndi ntcheto,*+Kapena mutu wake ndi mikondo yophera nsomba?