Yobu 42:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yobu atapempherera anzake aja,+ Yehova anathetsa mavuto a Yobu+ nʼkubwezeretsa chuma chimene anali nacho.* Yehova anamupatsa zonse zimene anali nazo, kuwirikiza kawiri.+
10 Yobu atapempherera anzake aja,+ Yehova anathetsa mavuto a Yobu+ nʼkubwezeretsa chuma chimene anali nacho.* Yehova anamupatsa zonse zimene anali nazo, kuwirikiza kawiri.+