-
Yobu 42:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Mʼdziko lonselo munalibe akazi okongola ngati ana aakazi a Yobu, ndipo bambo awo anawapatsa cholowa pamodzi ndi azichimwene awo.
-